Maliko 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo iwo anapita naye kwa Yesu. Koma mzimuwo utamuona, nthawi yomweyo unatsalimitsa mwanayo. Atagwa pansi anagubudukagubuduka ndi kuchita thovu.+
20 Pamenepo iwo anapita naye kwa Yesu. Koma mzimuwo utamuona, nthawi yomweyo unatsalimitsa mwanayo. Atagwa pansi anagubudukagubuduka ndi kuchita thovu.+