Maliko 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Chifukwa aliyense wokupatsani kapu+ ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ake a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ayi. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:41 Yesu—Ndi Njira, tsa. 150 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 8
41 Chifukwa aliyense wokupatsani kapu+ ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ake a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ayi.