Maliko 9:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Ndipo ngati dzanja lako limakuphunthwitsa, ulidule. Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi, kusiyana n’kupita ku Gehena,* kumoto umene sungazimitsidwe, uli ndi manja onse awiri.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:43 Yesu—Ndi Njira, tsa. 150 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, ptsa. 8-9
43 “Ndipo ngati dzanja lako limakuphunthwitsa, ulidule. Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi, kusiyana n’kupita ku Gehena,* kumoto umene sungazimitsidwe, uli ndi manja onse awiri.+