Maliko 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano kunafika Afarisi. Pofuna kumuyesa, anayamba kumufunsa ngati n’kololeka kuti mwamuna asiye mkazi wake.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 222 Nsanja ya Olonda,7/15/1989, tsa. 8
2 Tsopano kunafika Afarisi. Pofuna kumuyesa, anayamba kumufunsa ngati n’kololeka kuti mwamuna asiye mkazi wake.+