Maliko 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwe umadziwa malamulo akuti, ‘Usaphe munthu,*+ Usachite chigololo,+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama,+ Usachite chinyengo+ ndiponso lakuti Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:19 Nsanja ya Olonda,6/15/1986, ptsa. 8-9
19 Iwe umadziwa malamulo akuti, ‘Usaphe munthu,*+ Usachite chigololo,+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama,+ Usachite chinyengo+ ndiponso lakuti Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+