Maliko 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yesu anayang’ana uku ndi uku, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Zidzakhalatu zovuta kwambiri kuti anthu andalama+ adzalowe mu ufumu wa Mulungu!”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:23 Nsanja ya Olonda,6/15/1986, ptsa. 8-12
23 Yesu anayang’ana uku ndi uku, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Zidzakhalatu zovuta kwambiri kuti anthu andalama+ adzalowe mu ufumu wa Mulungu!”+