Maliko 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma Yakobo ndi Yohane, ana aamuna awiri a Zebedayo,+ anapita kwa iye ndi kumuuza kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutichitire chimene tikupempheni.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:35 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 228-229 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 8 Mawu a Mulungu, tsa. 89
35 Koma Yakobo ndi Yohane, ana aamuna awiri a Zebedayo,+ anapita kwa iye ndi kumuuza kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutichitire chimene tikupempheni.”+