Maliko 10:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako anafika mu Yeriko. Koma pamene iye ndi ophunzira ake ndi gulu lalikulu ndithu anali kutuluka mu Yeriko, Batimeyu, wopemphapempha komanso wakhungu (mwana wa Timeyu), anakhala pansi m’mphepete mwa msewu.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:46 Yesu—Ndi Njira, tsa. 230 Nsanja ya Olonda,5/1/2008, tsa. 319/15/1989, tsa. 82/1/1988, tsa. 5
46 Kenako anafika mu Yeriko. Koma pamene iye ndi ophunzira ake ndi gulu lalikulu ndithu anali kutuluka mu Yeriko, Batimeyu, wopemphapempha komanso wakhungu (mwana wa Timeyu), anakhala pansi m’mphepete mwa msewu.+