-
Maliko 14:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno Yesu ali ku Betaniya m’nyumba ya Simoni wakhate+ uja, ali pa chakudya, kunafika mayi wina ali ndi botolo lopangidwa ndi mwala wa alabasitala la mafuta onunkhira. Mafutawa anali nado weniweni, okwera mtengo kwambiri. Atatsegula botolo la alabasitala lija mochita kuswa, anayamba kuthira mafutawo m’mutu mwa Yesu.+
-