Maliko 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Poona izi, ena anakhumudwa ndi kunena kuti: “N’chifukwa chiyani akuwononga chonchi mafuta onunkhirawa?+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:4 Nsanja ya Olonda,4/15/2000, tsa. 31
4 Poona izi, ena anakhumudwa ndi kunena kuti: “N’chifukwa chiyani akuwononga chonchi mafuta onunkhirawa?+