Maliko 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti osaukawo muli nawo nthawi zonse,+ ndipo nthawi iliyonse imene mwafuna mungathe kuwachitira zabwino. Koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:7 Nsanja ya Olonda,9/15/1999, tsa. 5
7 Pakuti osaukawo muli nawo nthawi zonse,+ ndipo nthawi iliyonse imene mwafuna mungathe kuwachitira zabwino. Koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.+