Maliko 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Yudasi Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anachoka ndi kupita kwa ansembe aakulu kuti akapereke Yesu kwa iwo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:10 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 266-267 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 9
10 Kenako Yudasi Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anachoka ndi kupita kwa ansembe aakulu kuti akapereke Yesu kwa iwo.+