Maliko 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndi kumulonjeza kuti am’patsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino umene angamuperekere.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:11 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 266-267 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 9
11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndi kumulonjeza kuti am’patsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino umene angamuperekere.+