Maliko 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo m’nyumba imene akalowe, mukauze mwininyumbayo kuti, ‘Mphunzitsi akufunsa kuti: “Chipinda cha alendo chili kuti, mmene ine ndidyeremo pasika+ pamodzi ndi ophunzira anga?”’+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 267 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 9
14 ndipo m’nyumba imene akalowe, mukauze mwininyumbayo kuti, ‘Mphunzitsi akufunsa kuti: “Chipinda cha alendo chili kuti, mmene ine ndidyeremo pasika+ pamodzi ndi ophunzira anga?”’+