Maliko 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho atapita patsogolo pang’ono anadzigwetsa pansi ndipo anayamba kupemphera kuti ngati zikanatheka, asakumane ndi mayesero amenewa.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:35 Yesu—Ndi Njira, tsa. 282 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 8
35 Choncho atapita patsogolo pang’ono anadzigwetsa pansi ndipo anayamba kupemphera kuti ngati zikanatheka, asakumane ndi mayesero amenewa.+