Maliko 14:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Anabweranso kachitatu ndi kuwauza kuti: “Koma zoona nthawi ngati ino mukugona ndi kupumula! Basi! Nthawi yakwana!+ Taonani! Mwana wa munthu akuperekedwa m’manja mwa ochimwa.+
41 Anabweranso kachitatu ndi kuwauza kuti: “Koma zoona nthawi ngati ino mukugona ndi kupumula! Basi! Nthawi yakwana!+ Taonani! Mwana wa munthu akuperekedwa m’manja mwa ochimwa.+