Maliko 14:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pamenepo Yudasi anayenda molunjika ndi kufika kwa iye. Kenako anati: “Rabi!” Ndipo anam’psompsona.+
45 Pamenepo Yudasi anayenda molunjika ndi kufika kwa iye. Kenako anati: “Rabi!” Ndipo anam’psompsona.+