Maliko 14:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Tsiku ndi tsiku ndinali nanu m’kachisi kuphunzitsa,+ koma simunandigwire. Komabe, izi zikuchitika kuti Malemba+ akwaniritsidwe.”+
49 Tsiku ndi tsiku ndinali nanu m’kachisi kuphunzitsa,+ koma simunandigwire. Komabe, izi zikuchitika kuti Malemba+ akwaniritsidwe.”+