Maliko 14:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Koma Petulo, anali kum’tsatira chapatali ndithu,+ mpaka anafika m’bwalo lamkati kunyumba ya mkulu wa ansembe. Kumeneko iye anakhala pansi pamodzi ndi antchito a m’nyumbamo, n’kumawotha moto walawilawi. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:54 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Tsanzirani, tsa. 200 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, tsa. 2311/15/1990, tsa. 8
54 Koma Petulo, anali kum’tsatira chapatali ndithu,+ mpaka anafika m’bwalo lamkati kunyumba ya mkulu wa ansembe. Kumeneko iye anakhala pansi pamodzi ndi antchito a m’nyumbamo, n’kumawotha moto walawilawi.
14:54 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Tsanzirani, tsa. 200 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, tsa. 2311/15/1990, tsa. 8