Maliko 14:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Potsirizira pake, mkulu wa ansembe anaimirira pakati pawo ndi kufunsa Yesu kuti: “Sukuyankha chilichonse? Kodi n’zoona zimene awa akukunenezazi?”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:60 Nsanja ya Olonda,4/1/2011, ptsa. 19-21
60 Potsirizira pake, mkulu wa ansembe anaimirira pakati pawo ndi kufunsa Yesu kuti: “Sukuyankha chilichonse? Kodi n’zoona zimene awa akukunenezazi?”+