Maliko 14:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Mwadzimvera nokha mmene akunyozera Mulungu.+ Mukuona bwanji pamenepa?” Onse anati ayenera kuphedwa basi. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:64 Yesu—Ndi Njira, tsa. 290
64 Mwadzimvera nokha mmene akunyozera Mulungu.+ Mukuona bwanji pamenepa?” Onse anati ayenera kuphedwa basi.