Maliko 14:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma iye anakana kuti: “Ngakhale kumudziwa, sindikumudziwa ameneyo, ndipo sindikumvetsa kuti ukunena chiyani.” Atatero anatuluka panja ndi kupita kukachipinda ka kuchipata.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:68 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
68 Koma iye anakana kuti: “Ngakhale kumudziwa, sindikumudziwa ameneyo, ndipo sindikumvetsa kuti ukunena chiyani.” Atatero anatuluka panja ndi kupita kukachipinda ka kuchipata.+