Maliko 14:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Apanso anakana. Patapitanso kanthawi pang’ono, amene anali ataimirira chapafupi anayamba kuuza Petulo kuti: “Ndithu iwenso uli m’gulu la ophunzira ake. Ndipo ndiwenso Mgalileya.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:70 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
70 Apanso anakana. Patapitanso kanthawi pang’ono, amene anali ataimirira chapafupi anayamba kuuza Petulo kuti: “Ndithu iwenso uli m’gulu la ophunzira ake. Ndipo ndiwenso Mgalileya.”+