Maliko 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Pilato, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo,+ anawamasulira Baraba. Ndipo atalamula kuti Yesu amukwapule, anamupereka kuti akamupachike.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 294 Nsanja ya Olonda,1/1/1991, tsa. 9
15 Pamenepo Pilato, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo,+ anawamasulira Baraba. Ndipo atalamula kuti Yesu amukwapule, anamupereka kuti akamupachike.+