Maliko 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano anayamba kum’lonjera kuti: “Mtendere ukhale nanu,+ inu Mfumu ya Ayuda!”