Maliko 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho anafika naye kumalo otchedwa Gologota. Liwuli akalimasulira, limatanthauza Malo a Chibade.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:22 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 30-31
22 Choncho anafika naye kumalo otchedwa Gologota. Liwuli akalimasulira, limatanthauza Malo a Chibade.+