Maliko 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno mawu osonyeza mlandu wake+ anawalemba pamwamba pake kuti: “Mfumu ya Ayuda.”+