Maliko 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Komanso iwo anapachika achifwamba awiri limodzi ndi iye. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja, wina kumanzere kwake.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:27 Nsanja ya Olonda,2/1/2012, tsa. 14
27 Komanso iwo anapachika achifwamba awiri limodzi ndi iye. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja, wina kumanzere kwake.+