Maliko 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu amene anali kudutsa pamenepo anali kumulankhula monyoza.+ Anali kupukusa mitu yawo n’kumanena kuti: “Iwe wogwetsa kachisi ndi kum’manga m’masiku atatu,+
29 Anthu amene anali kudutsa pamenepo anali kumulankhula monyoza.+ Anali kupukusa mitu yawo n’kumanena kuti: “Iwe wogwetsa kachisi ndi kum’manga m’masiku atatu,+