Maliko 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tsopano ena mwa anthu amene anaimirira chapafupi, atamva zimenezo, anayamba kunena kuti: “Tamverani! Akuitana Eliya.”+
35 Tsopano ena mwa anthu amene anaimirira chapafupi, atamva zimenezo, anayamba kunena kuti: “Tamverani! Akuitana Eliya.”+