Maliko 15:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 amene anali kuyenda naye limodzi+ ndi kumutumikira pamene anali ku Galileya. Panalinso amayi ena ambiri amene anabwera naye limodzi kuchokera ku Yerusalemu.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:41 Nsanja ya Olonda,8/15/2015, tsa. 30
41 amene anali kuyenda naye limodzi+ ndi kumutumikira pamene anali ku Galileya. Panalinso amayi ena ambiri amene anabwera naye limodzi kuchokera ku Yerusalemu.+