Luka 1:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Izi zachitika chifukwa zimene Mulungu wanena, sizilephereka.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:37 Kufotokoza Mavesi a m’Baibulo, article 53 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Gabirieli ananeneratu za kubadwa kwa Yesu (gnj 1 13:52–18:26)