Luka 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Poyankha iye anali kuwauza kuti: “Munthu amene ali ndi malaya awiri amkati agawireko munthu amene alibiretu. Amenenso ali ndi chakudya achite chimodzimodzi.”+
11 Poyankha iye anali kuwauza kuti: “Munthu amene ali ndi malaya awiri amkati agawireko munthu amene alibiretu. Amenenso ali ndi chakudya achite chimodzimodzi.”+