Luka 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Malemba amati, ‘Yehova* Mulungu wako+ ndi amene uyenera kumulambira, ndipo uyenera kutumikira iye yekha basi.’”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:8 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 58 Nsanja ya Olonda,5/1/1996, tsa. 95/1/1989, tsa. 18
8 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Malemba amati, ‘Yehova* Mulungu wako+ ndi amene uyenera kumulambira, ndipo uyenera kutumikira iye yekha basi.’”+