Luka 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso, anayamba kuphunzitsa m’masunagoge awo, ndipo anthu onse anali kumulemekeza.+