-
Luka 4:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Atatero anapinda mpukutuwo, n’kuubwezera kwa wotumikira mmenemo ndi kukhala pansi. Maso onse m’sunagogemo anali pa iye kumuyang’anitsitsa.
-