Luka 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsiku lina pa sabata, Yesu anali kudutsa m’munda wa tirigu, ndipo ophunzira ake anali kubudula+ ngala za tirigu. Anali kuzifikisa m’manja mwawo n’kumadya.+
6 Tsiku lina pa sabata, Yesu anali kudutsa m’munda wa tirigu, ndipo ophunzira ake anali kubudula+ ngala za tirigu. Anali kuzifikisa m’manja mwawo n’kumadya.+