Luka 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Alembi ndi Afarisi anali kumuyang’anitsitsa+ tsopano, kuti aone ngati angachiritse munthu pa sabata. Iwo anali n’cholinga chakuti am’peze chifukwa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,1/1/1987, tsa. 14
7 Alembi ndi Afarisi anali kumuyang’anitsitsa+ tsopano, kuti aone ngati angachiritse munthu pa sabata. Iwo anali n’cholinga chakuti am’peze chifukwa.+