Luka 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Tsoka inu amene mukukhuta tsopano, chifukwa mudzamva njala.+ “Tsoka inu amene mukuseka tsopano, chifukwa mudzamva chisoni ndi kulira.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:25 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 85-86 Nsanja ya Olonda,3/15/1987, tsa. 11
25 “Tsoka inu amene mukukhuta tsopano, chifukwa mudzamva njala.+ “Tsoka inu amene mukuseka tsopano, chifukwa mudzamva chisoni ndi kulira.+