Luka 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chabwino+ cha mtima wake. Koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa, pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:45 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 51 Nsanja ya Olonda,10/15/2001, ptsa. 23-24
45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chabwino+ cha mtima wake. Koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa, pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+