Luka 6:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Iyeyo ali ngati munthu womanga nyumba, amene anakumba mozama kwambiri ndi kuyala maziko pathanthwe. Ndipo pamene mtsinje unasefukira,+ madzi anawomba nyumbayo, koma sanathe kuigwedeza, chifukwa anaimanga bwino.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:48 Nsanja ya Olonda,11/1/2008, ptsa. 29-311/1/2007, tsa. 3210/1/1990, tsa. 24
48 Iyeyo ali ngati munthu womanga nyumba, amene anakumba mozama kwambiri ndi kuyala maziko pathanthwe. Ndipo pamene mtsinje unasefukira,+ madzi anawomba nyumbayo, koma sanathe kuigwedeza, chifukwa anaimanga bwino.+