6 Choncho Yesu ananyamuka nawo limodzi. Koma atatsala pang’ono kufika kunyumbako, anakumana ndi mabwenzi a kapitawo wa asilikali uja, amene anawatuma kuti adzamuuze kuti: “Mbuyanga, musavutike, pakuti ine sindili woyenera kuti inu mulowe m’nyumba mwanga.+