Luka 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yesu atamva zimenezi anadabwa ndi munthu ameneyu. Kenako anacheukira khamu la anthu omutsatira aja n’kunena kuti: “Kunena zoona, ngakhale mu Isiraeli sindinapezemo chikhulupiriro chachikulu ngati chimenechi.”+
9 Yesu atamva zimenezi anadabwa ndi munthu ameneyu. Kenako anacheukira khamu la anthu omutsatira aja n’kunena kuti: “Kunena zoona, ngakhale mu Isiraeli sindinapezemo chikhulupiriro chachikulu ngati chimenechi.”+