Luka 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma amene anatumidwa aja atabwerera kunyumba, anapeza kapolo uja ali bwinobwino.+