Luka 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mu ola limenelo iye anachiritsa nthenda zambiri+ ndi anthu ambiri odwala mwakayakaya ndi kutulutsa mizimu yoipa. Ndipo anachiritsa akhungu ochuluka moti anayamba kuona.
21 Mu ola limenelo iye anachiritsa nthenda zambiri+ ndi anthu ambiri odwala mwakayakaya ndi kutulutsa mizimu yoipa. Ndipo anachiritsa akhungu ochuluka moti anayamba kuona.