Luka 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Amithenga a Yohane aja atachoka, iye anayamba kuuza khamu la anthulo za Yohane kuti: “Kodi munapita m’chipululu kukaona chiyani? Kodi munapita kukaona bango logwedezeka ndi mphepo?+
24 Amithenga a Yohane aja atachoka, iye anayamba kuuza khamu la anthulo za Yohane kuti: “Kodi munapita m’chipululu kukaona chiyani? Kodi munapita kukaona bango logwedezeka ndi mphepo?+