Luka 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 (Pamenepo anthu onse ndi okhometsa msonkho omwe atamva zimenezi, analengeza kuti Mulungu ndi wolungama,+ popeza iwo anali atabatizidwa ndi ubatizo wa Yohane.+
29 (Pamenepo anthu onse ndi okhometsa msonkho omwe atamva zimenezi, analengeza kuti Mulungu ndi wolungama,+ popeza iwo anali atabatizidwa ndi ubatizo wa Yohane.+