Luka 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma mayi wina amene anali wodziwika mumzindawo kuti ndi wochimwa, anamva kuti Yesu akudya chakudya m’nyumba ya Mfarisi. Choncho anapita komweko ndi botolo lopangidwa ndi mwala wa alabasitala,+ muli mafuta onunkhira. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:37 Nsanja ya Olonda,8/15/2010, tsa. 612/15/2001, tsa. 17
37 Koma mayi wina amene anali wodziwika mumzindawo kuti ndi wochimwa, anamva kuti Yesu akudya chakudya m’nyumba ya Mfarisi. Choncho anapita komweko ndi botolo lopangidwa ndi mwala wa alabasitala,+ muli mafuta onunkhira.