Luka 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mfarisi amene anamuitana uja ataona izi, mumtima mwake anati: “Munthu uyu akanakhala mneneri,+ akanadziwa kuti mkazi amene akumugwirayu ndi ndani, ndiponso kuti ndi wotani. Akanadziwa kuti ndi wochimwa.”+
39 Mfarisi amene anamuitana uja ataona izi, mumtima mwake anati: “Munthu uyu akanakhala mneneri,+ akanadziwa kuti mkazi amene akumugwirayu ndi ndani, ndiponso kuti ndi wotani. Akanadziwa kuti ndi wochimwa.”+