Luka 7:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuza kuti, machimo ake akhululukidwa,+ ngakhale kuti ndi ochuluka. N’chifukwa chake akusonyeza chikondi chochuluka. Koma amene wakhululukidwa machimo ochepa amasonyezanso chikondi chochepa.” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:47 Yesu—Ndi Njira, tsa. 100 Nsanja ya Olonda,8/1/1987, tsa. 9
47 Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuza kuti, machimo ake akhululukidwa,+ ngakhale kuti ndi ochuluka. N’chifukwa chake akusonyeza chikondi chochuluka. Koma amene wakhululukidwa machimo ochepa amasonyezanso chikondi chochepa.”